Mateyu 16:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma iye anatembenuka n’kuuza Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga, Satana!+ Ndiwe chopunthwitsa kwa ine, chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu,+ koma maganizo a anthu.”
23 Koma iye anatembenuka n’kuuza Petulo kuti: “Pita kumbuyo kwanga, Satana!+ Ndiwe chopunthwitsa kwa ine, chifukwa zimene umaganiza si maganizo a Mulungu,+ koma maganizo a anthu.”