Aroma 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano, Mulungu amene amatipatsa mphamvu kuti tithe kupirira ndiponso amene amatitonthoza, achititse nonsenu kukhala ndi maganizo+ amene Khristu Yesu anali nawo, Afilipi 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Khalani ndi maganizo amenewa, amenenso Khristu Yesu anali nawo.+
5 Tsopano, Mulungu amene amatipatsa mphamvu kuti tithe kupirira ndiponso amene amatitonthoza, achititse nonsenu kukhala ndi maganizo+ amene Khristu Yesu anali nawo,