Yesaya 54:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ngati aliyense atakuukira, sadzakhala atatumidwa ndi ine.+ Aliyense wokuukira adzagwa chifukwa cha iwe.”+ 2 Atesalonika 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chiweruzo cha Mulunguchi n’cholungama chifukwa akubwezera masautso kwa amene amakusautsani.+
15 Ngati aliyense atakuukira, sadzakhala atatumidwa ndi ine.+ Aliyense wokuukira adzagwa chifukwa cha iwe.”+