Mlaliki 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndi bwino kukhala ndi nzeru kuposa kukhala ndi zida zomenyera nkhondo, ndipo wochimwa mmodzi yekha akhoza kuwononga zabwino zochuluka.+ 1 Akorinto 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Musasocheretsedwe. Kugwirizana ndi anthu oipa kumawononga makhalidwe abwino.+
18 Ndi bwino kukhala ndi nzeru kuposa kukhala ndi zida zomenyera nkhondo, ndipo wochimwa mmodzi yekha akhoza kuwononga zabwino zochuluka.+