Ekisodo 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa kwa masiku 7.+ Musamadzapezeke ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+ Mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa usamadzapezeke pena paliponse m’dziko lanu.+
7 Muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa kwa masiku 7.+ Musamadzapezeke ndi chilichonse chokhala ndi chofufumitsa.+ Mtanda wa ufa wokanda wokhala ndi chofufumitsa usamadzapezeke pena paliponse m’dziko lanu.+