Mateyu 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pamenepo anazindikira kuti sakunena kuti asamale ndi zofufumitsa mitanda ya mkate, koma kuti asamale ndi zimene Afarisi ndi Asaduki amaphunzitsa.+
12 Pamenepo anazindikira kuti sakunena kuti asamale ndi zofufumitsa mitanda ya mkate, koma kuti asamale ndi zimene Afarisi ndi Asaduki amaphunzitsa.+