Mateyu 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Akapanda kuwamvera amenewanso, uuze mpingo. Ndipo akapandanso kumvera mpingowo, kwa iwe akhale ngati munthu wochokera mu mtundu wina+ komanso ngati wokhometsa msonkho.+
17 Akapanda kuwamvera amenewanso, uuze mpingo. Ndipo akapandanso kumvera mpingowo, kwa iwe akhale ngati munthu wochokera mu mtundu wina+ komanso ngati wokhometsa msonkho.+