Aroma 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa ngati tagwirizana naye pokhala ndi imfa yofanana ndi yake,+ ndithudi tidzagwirizananso naye poukitsidwa mofanana ndi iye.+ Aroma 8:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chotero, mzimu wa amene anaukitsa Yesu kwa akufa ukakhala mwa inu, iye amene anaukitsa Khristu Yesu kwa akufa+ adzachititsanso matupi anu otha kufawo kukhala ndi moyo+ mwa mzimu wake umene ukukhala mwa inu. 2 Akorinto 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 podziwa kuti amene anaukitsa Yesu adzaukitsanso ifeyo pamodzi ndi Yesu, ndipo adzatipititsa pamaso pa Yesuyo pamodzi ndi inuyo.+
5 Chifukwa ngati tagwirizana naye pokhala ndi imfa yofanana ndi yake,+ ndithudi tidzagwirizananso naye poukitsidwa mofanana ndi iye.+
11 Chotero, mzimu wa amene anaukitsa Yesu kwa akufa ukakhala mwa inu, iye amene anaukitsa Khristu Yesu kwa akufa+ adzachititsanso matupi anu otha kufawo kukhala ndi moyo+ mwa mzimu wake umene ukukhala mwa inu.
14 podziwa kuti amene anaukitsa Yesu adzaukitsanso ifeyo pamodzi ndi Yesu, ndipo adzatipititsa pamaso pa Yesuyo pamodzi ndi inuyo.+