Genesis 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+ Mateyu 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 n’kunena kuti, ‘Pa chifukwa chimenechi mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi’?+ Aefeso 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake, n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi.”+
24 Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake,+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo iwo adzakhala thupi limodzi.+
5 n’kunena kuti, ‘Pa chifukwa chimenechi mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake+ n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi’?+
31 “Pa chifukwa chimenechi, mwamuna adzasiya bambo ake ndi mayi ake, n’kudziphatika kwa mkazi wake, ndipo awiriwo adzakhala thupi limodzi.”+