1 Akorinto 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mkazi asachite ulamuliro pathupi lake. Ulamulirowo ukhale ndi mwamuna wake.+ Mwamunanso asachite ulamuliro pathupi lake, koma ulamulirowo ukhale ndi mkazi wake.+
4 Mkazi asachite ulamuliro pathupi lake. Ulamulirowo ukhale ndi mwamuna wake.+ Mwamunanso asachite ulamuliro pathupi lake, koma ulamulirowo ukhale ndi mkazi wake.+