1 Akorinto 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Timalankhulanso zinthu zimenezi, osati ndi mawu ophunzitsidwa ndi nzeru za anthu,+ koma ndi mawu amene mzimu+ watiphunzitsa, pamene tikuphatikiza zochitika zauzimu ndi mawu auzimu.+ Agalatiya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti ndikufuna mudziwe, abale, kuti uthenga wabwino umene ndinaulengeza monga uthenga wabwino sunachokere kwa anthu.+
13 Timalankhulanso zinthu zimenezi, osati ndi mawu ophunzitsidwa ndi nzeru za anthu,+ koma ndi mawu amene mzimu+ watiphunzitsa, pamene tikuphatikiza zochitika zauzimu ndi mawu auzimu.+
11 Pakuti ndikufuna mudziwe, abale, kuti uthenga wabwino umene ndinaulengeza monga uthenga wabwino sunachokere kwa anthu.+