Mateyu 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero inenso ndikukuuza kuti, Iwe ndiwe Petulo,+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Zipata za Manda+ sizidzaugonjetsa.+ 1 Petulo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+
18 Chotero inenso ndikukuuza kuti, Iwe ndiwe Petulo,+ ndipo pathanthwe+ ili ndidzamangapo mpingo wanga. Zipata za Manda+ sizidzaugonjetsa.+
4 Pamene mukubwera kwa iye, amene ndiye mwala wamoyo+ umene anthu+ anaukana,+ koma umene Mulungu anausankha, umenenso uli wamtengo wapatali kwa iye,+