Danieli 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “‘Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu a padziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa oyera a Wamkulukulu.+ Ufumu wawo+ udzakhalapo mpaka kalekale ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’+ 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
27 “‘Ufumu, ulamuliro, ndi ulemerero wa maufumu a padziko lonse lapansi zinaperekedwa kwa oyera a Wamkulukulu.+ Ufumu wawo+ udzakhalapo mpaka kalekale ndipo maulamuliro onse adzawatumikira ndi kuwamvera.’+