Deuteronomo 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 pamenepo uzim’tenga ndi kulowa naye m’nyumba yako. Kenako azimeta tsitsi lake+ ndi kusamalira zikhadabo zake.
12 pamenepo uzim’tenga ndi kulowa naye m’nyumba yako. Kenako azimeta tsitsi lake+ ndi kusamalira zikhadabo zake.