Maliko 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Kenako adzaona Mwana wa munthu+ akubwera m’mitambo ndi mphamvu yaikulu ndiponso ulemerero.+