Aroma 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngati tili ndi mphatso ya utumiki, tiyeni tichitebe utumikiwo.+ Amene akuphunzitsa,+ aziphunzitsa ndithu.+ Aefeso 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo anapereka ena monga atumwi,+ ena monga aneneri,+ ena monga alaliki,*+ ena monga abusa ndi aphunzitsi,+
7 Ngati tili ndi mphatso ya utumiki, tiyeni tichitebe utumikiwo.+ Amene akuphunzitsa,+ aziphunzitsa ndithu.+
11 Ndipo anapereka ena monga atumwi,+ ena monga aneneri,+ ena monga alaliki,*+ ena monga abusa ndi aphunzitsi,+