1 Akorinto 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera,+ yodziwa zinsinsi zonse zopatulika,+ yodziwa zinthu zonse,+ komanso ngati ndili ndi chikhulupiriro chonse choti n’kusuntha nacho mapiri,+ koma ndilibe chikondi, sindili kanthu.+ 2 Akorinto 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano, popeza tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi umene anaunena kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, chotero ndinalankhula,”+ ifenso tili ndi chikhulupiriro, chotero tikulankhula,
2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera,+ yodziwa zinsinsi zonse zopatulika,+ yodziwa zinthu zonse,+ komanso ngati ndili ndi chikhulupiriro chonse choti n’kusuntha nacho mapiri,+ koma ndilibe chikondi, sindili kanthu.+
13 Tsopano, popeza tili ndi mtima wachikhulupiriro wofanana ndi umene anaunena kuti: “Ndinali ndi chikhulupiriro, chotero ndinalankhula,”+ ifenso tili ndi chikhulupiriro, chotero tikulankhula,