1 Akorinto 14:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno zizikhala bwanji, abale? Mukasonkhana pamodzi, wina amakhala ndi salimo, wina chiphunzitso, wina mawu amene walandira kuchokera kwa Mulungu, wina lilime lachilendo, wina kumasulira.+ Zochitika zonse zikhale zolimbikitsa.+
26 Ndiyeno zizikhala bwanji, abale? Mukasonkhana pamodzi, wina amakhala ndi salimo, wina chiphunzitso, wina mawu amene walandira kuchokera kwa Mulungu, wina lilime lachilendo, wina kumasulira.+ Zochitika zonse zikhale zolimbikitsa.+