Genesis 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero maso awo anatseguka, ndipo anazindikira kuti ali maliseche.+ Choncho anadzisokera masamba a mkuyu n’kupanga zovala zomangira m’chiuno.+ Genesis 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako Yehova Mulungu anapangira Adamu ndi mkazi wake zovala zazitali zachikopa, n’kuwaveka.+ 2 Timoteyo 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’nyumba yaikulu simukhala ziwiya zagolide ndi zasiliva zokha ayi, koma mumakhalanso zamtengo ndi zadothi. Ziwiya zina zimakhala za ntchito yolemekezeka koma zina zimakhala za ntchito yonyozeka.+
7 Atatero maso awo anatseguka, ndipo anazindikira kuti ali maliseche.+ Choncho anadzisokera masamba a mkuyu n’kupanga zovala zomangira m’chiuno.+
20 M’nyumba yaikulu simukhala ziwiya zagolide ndi zasiliva zokha ayi, koma mumakhalanso zamtengo ndi zadothi. Ziwiya zina zimakhala za ntchito yolemekezeka koma zina zimakhala za ntchito yonyozeka.+