Aroma 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti n’chapatali kuti munthu wina afere munthu wolungama.+ Zoonadi, mwina wina angalimbe mtima kufera+ munthu wabwino.+
7 Pakuti n’chapatali kuti munthu wina afere munthu wolungama.+ Zoonadi, mwina wina angalimbe mtima kufera+ munthu wabwino.+