1 Atesalonika 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse. 2 Petulo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuwonjezera apo, muone kuleza mtima kwa Ambuye wathu kukhala chipulumutso, monganso mmene m’bale wathu wokondedwa Paulo anakulemberani mogwirizana ndi nzeru+ zimene anapatsidwa.+
14 Komanso tikukudandaulirani abale kuti, langizani ochita zosalongosoka,+ lankhulani molimbikitsa kwa amtima wachisoni,+ thandizani ofooka, khalani oleza+ mtima kwa onse.
15 Kuwonjezera apo, muone kuleza mtima kwa Ambuye wathu kukhala chipulumutso, monganso mmene m’bale wathu wokondedwa Paulo anakulemberani mogwirizana ndi nzeru+ zimene anapatsidwa.+