Mateyu 22:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iye anamuyankha kuti: “‘Uzikonda Yehova* Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, ndi maganizo ako onse.’+ Aroma 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chikondi+ sichilimbikitsa munthu kuchitira zoipa mnzake,+ chotero chilamulo chimakwaniritsidwa m’chikondi.+
37 Iye anamuyankha kuti: “‘Uzikonda Yehova* Mulungu wako ndi mtima wako wonse, moyo wako wonse, ndi maganizo ako onse.’+
10 Chikondi+ sichilimbikitsa munthu kuchitira zoipa mnzake,+ chotero chilamulo chimakwaniritsidwa m’chikondi.+