1 Akorinto 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ndikanakonda kuti nonsenu muzilankhula malilime,+ koma ndikuona kuti ndi bwino kuti muzinenera.+ Ndithudi, wonenera amaposa wolankhula malilime achilendo,+ kupatulapo ngati wa malilimeyo amasulira, kuti amange mpingo.
5 Tsopano ndikanakonda kuti nonsenu muzilankhula malilime,+ koma ndikuona kuti ndi bwino kuti muzinenera.+ Ndithudi, wonenera amaposa wolankhula malilime achilendo,+ kupatulapo ngati wa malilimeyo amasulira, kuti amange mpingo.