1 Akorinto 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera,+ yodziwa zinsinsi zonse zopatulika,+ yodziwa zinthu zonse,+ komanso ngati ndili ndi chikhulupiriro chonse choti n’kusuntha nacho mapiri,+ koma ndilibe chikondi, sindili kanthu.+
2 Ndipo ngati ndili ndi mphatso yonenera,+ yodziwa zinsinsi zonse zopatulika,+ yodziwa zinthu zonse,+ komanso ngati ndili ndi chikhulupiriro chonse choti n’kusuntha nacho mapiri,+ koma ndilibe chikondi, sindili kanthu.+