1 Akorinto 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ngakhale zili choncho, ndi bwino kuti mumpingo ndilankhule mawu asanu omveka, kutinso ndilangize ena ndi mawuwo, kusiyana n’kulankhula mawu 10,000 m’lilime lachilendo.+
19 Ngakhale zili choncho, ndi bwino kuti mumpingo ndilankhule mawu asanu omveka, kutinso ndilangize ena ndi mawuwo, kusiyana n’kulankhula mawu 10,000 m’lilime lachilendo.+