1 Akorinto 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano abale, ponena za mphatso zauzimu,+ sindikufuna kuti mukhale osadziwa. 1 Akorinto 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano ntchito za mzimu zimapatsidwa kwa munthu aliyense pa cholinga chopindulitsa.+