1 Akorinto 12:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 M’malomwake, pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zazikulu.+ Komabe, ine ndikuonetsani njira yopambana.+ 1 Atesalonika 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Musanyoze mawu aulosi.+
31 M’malomwake, pitirizani kufunafuna mwachangu mphatso zazikulu.+ Komabe, ine ndikuonetsani njira yopambana.+