Yohane 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano patapita masiku 8, ophunzira akewo analinso m’nyumba, ndipo Tomasi anali nawo pamodzi. Yesu anafika ngakhale kuti zitseko zinali zokhoma. Iye anaimirira pakati pawo ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+
26 Tsopano patapita masiku 8, ophunzira akewo analinso m’nyumba, ndipo Tomasi anali nawo pamodzi. Yesu anafika ngakhale kuti zitseko zinali zokhoma. Iye anaimirira pakati pawo ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+