Afilipi 3:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iyeyo adzakonzanso thupi lathu lonyozekali+ kuti lifanane ndi thupi lake laulemerero.+ Adzatero malinga ndi mphamvu+ imene ali nayo, yotha kugonjetsera+ ngakhale zinthu zonse kwa iye mwini.
21 Iyeyo adzakonzanso thupi lathu lonyozekali+ kuti lifanane ndi thupi lake laulemerero.+ Adzatero malinga ndi mphamvu+ imene ali nayo, yotha kugonjetsera+ ngakhale zinthu zonse kwa iye mwini.