Aroma 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndikuperekanso moni ku mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo.+ Moni kwa wokondedwa wanga Epeneto, amene ndi chipatso choyambirira+ cha Khristu mu Asia.
5 Ndikuperekanso moni ku mpingo umene umasonkhana m’nyumba mwawo.+ Moni kwa wokondedwa wanga Epeneto, amene ndi chipatso choyambirira+ cha Khristu mu Asia.