Ekisodo 34:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma Mose akamalowa kukaonekera kwa Yehova kuti akalankhule naye, anali kuchotsa chophimbacho mpaka atatulukamo.+ Kenako anali kupita kwa ana a Isiraeli ndi kuwauza zimene walamulidwa.+ Aroma 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iwonso ngati angayambe kukhala ndi chikhulupiriro, adzalumikizidwa kumtengowo,+ pakuti Mulungu akhoza kuwalumikizanso. Aroma 11:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+
34 Koma Mose akamalowa kukaonekera kwa Yehova kuti akalankhule naye, anali kuchotsa chophimbacho mpaka atatulukamo.+ Kenako anali kupita kwa ana a Isiraeli ndi kuwauza zimene walamulidwa.+
23 Iwonso ngati angayambe kukhala ndi chikhulupiriro, adzalumikizidwa kumtengowo,+ pakuti Mulungu akhoza kuwalumikizanso.
26 Mwa njira imeneyi, Aisiraeli onse+ adzapulumuka. Izi zikugwirizana ndi zimene Malemba amanena kuti: “Wolanditsa adzachokera m’Ziyoni+ ndi kuchotsera Yakobo zochita zonse zosalemekeza Mulungu.+