2 Akorinto 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti pamaso pa Mulungu ndife fungo lonunkhira bwino+ lonena za uthenga wa Khristu, limene likumvedwa ndi anthu amene akupita kukapulumuka komanso ndi amene akupita kukawonongedwa.+
15 Pakuti pamaso pa Mulungu ndife fungo lonunkhira bwino+ lonena za uthenga wa Khristu, limene likumvedwa ndi anthu amene akupita kukapulumuka komanso ndi amene akupita kukawonongedwa.+