Genesis 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Mulungu anati:+ “Pakhale kuwala.” Ndipo kuwala kunakhalapo.+