2 Akorinto 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Popeza tili ndi utumiki umenewu+ malinga ndi chifundo chimene tinasonyezedwa,+ sitikubwerera m’mbuyo.
4 Popeza tili ndi utumiki umenewu+ malinga ndi chifundo chimene tinasonyezedwa,+ sitikubwerera m’mbuyo.