Aefeso 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 ndi kukula kwa mphamvu zake zopambana+ zimene wazipereka kwa ife okhulupirira. Kukula kumeneko n’kogwirizana ndi ntchito+ ya mphamvu yake yodabwitsa,
19 ndi kukula kwa mphamvu zake zopambana+ zimene wazipereka kwa ife okhulupirira. Kukula kumeneko n’kogwirizana ndi ntchito+ ya mphamvu yake yodabwitsa,