1 Akorinto 15:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Limafesedwa lonyozeka,+ limaukitsidwa mu ulemerero.+ Limafesedwa lofooka,+ limaukitsidwa mu mphamvu.+ Afilipi 1:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti kwa ine, ndikakhala moyo, ndikhalira moyo Khristu,+ ndipo ndikamwalira+ ndipindula.
43 Limafesedwa lonyozeka,+ limaukitsidwa mu ulemerero.+ Limafesedwa lofooka,+ limaukitsidwa mu mphamvu.+