Machitidwe 13:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Chotero dziwani abale anga kuti, ife tikulalikira kwa inu za kukhululukidwa kwa machimo kudzera mwa Iyeyu.+
38 “Chotero dziwani abale anga kuti, ife tikulalikira kwa inu za kukhululukidwa kwa machimo kudzera mwa Iyeyu.+