Machitidwe 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chotero Petulo anakhala akusungidwa m’ndendemo, koma mpingo unali kumupempherera+ mosalekeza kwa Mulungu ndi mtima wonse.
5 Chotero Petulo anakhala akusungidwa m’ndendemo, koma mpingo unali kumupempherera+ mosalekeza kwa Mulungu ndi mtima wonse.