Machitidwe 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”
23 Pamene anali kuyang’anitsitsa Khoti Lalikulu la Ayudalo, Paulo anati: “Amuna inu, abale anga, ndachita zinthu popanda chikumbumtima changa kunditsutsa ngakhale pang’ono pamaso pa Mulungu+ mpaka lero.”