Mateyu 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Pakuti Malemba amati, ‘Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira,+ ndipo uyenera kutumikira+ iye yekha basi.’”+ Chivumbulutso 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo kumwamba kunabuka nkhondo: Mikayeli+ ndi angelo ake anamenyana ndi chinjoka. Chinjokacho ndi angelo ake chinamenya nkhondo,
10 Koma Yesu anamuyankha kuti: “Choka Satana! Pakuti Malemba amati, ‘Yehova Mulungu wako ndi amene uyenera kumulambira,+ ndipo uyenera kutumikira+ iye yekha basi.’”+
7 Ndipo kumwamba kunabuka nkhondo: Mikayeli+ ndi angelo ake anamenyana ndi chinjoka. Chinjokacho ndi angelo ake chinamenya nkhondo,