Aroma 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo. 2 Akorinto 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malo sakukucheperani mumtima mwathu,+ koma m’chikondi chanu ndi mmene muli malo ochepa.+
10 Pokonda abale,+ khalani ndi chikondi chenicheni pakati panu. Posonyezana ulemu,+ khalani patsogolo.