Afilipi 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ngakhale kuti ndikudzipereka ngati nsembe yachakumwa imene ikuthiridwa+ pansembe+ ndi pa ntchito yotumikira anthu imene chikhulupiriro chakupatsani,+ ndine wokondwa ndipo ndikukondwera+ ndi inu nonse. Filimoni 7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chikondi chako m’bale chandisangalatsa ndi kundilimbikitsa kwambiri,+ chifukwa walimbikitsanso mitima ya oyera.+
17 Ngakhale kuti ndikudzipereka ngati nsembe yachakumwa imene ikuthiridwa+ pansembe+ ndi pa ntchito yotumikira anthu imene chikhulupiriro chakupatsani,+ ndine wokondwa ndipo ndikukondwera+ ndi inu nonse.
7 Chikondi chako m’bale chandisangalatsa ndi kundilimbikitsa kwambiri,+ chifukwa walimbikitsanso mitima ya oyera.+