Machitidwe 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Chotero lapa choipa chakochi, ndipo upemphe kwa Yehova mopembedzera+ kuti ngati n’kotheka, maganizo oipa a mtima wakowo akhululukidwe.
22 Chotero lapa choipa chakochi, ndipo upemphe kwa Yehova mopembedzera+ kuti ngati n’kotheka, maganizo oipa a mtima wakowo akhululukidwe.