1 Akorinto 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Tsopano kunena za amene sali pabanja,* ndilibe lamulo lililonse la Ambuye, koma ndikupereka maganizo anga+ monga munthu amene ndinasonyezedwa chifundo ndi Ambuye+ kuti ndikhale wokhulupirika.+
25 Tsopano kunena za amene sali pabanja,* ndilibe lamulo lililonse la Ambuye, koma ndikupereka maganizo anga+ monga munthu amene ndinasonyezedwa chifundo ndi Ambuye+ kuti ndikhale wokhulupirika.+