Aroma 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma tikuyamika Mulungu kuti ngakhale poyamba munali akapolo a uchimo, munamvera mochokera pansi pa mtima mtundu wa chiphunzitso chimene chinaperekedwa kwa inu.+ 2 Akorinto 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiponso iyeyo amakukondani kwambiri nonsenu akakumbukira kumvera kwanu,+ komanso mmene munamulandirira ndi mantha ndiponso kunjenjemera.
17 Koma tikuyamika Mulungu kuti ngakhale poyamba munali akapolo a uchimo, munamvera mochokera pansi pa mtima mtundu wa chiphunzitso chimene chinaperekedwa kwa inu.+
15 Ndiponso iyeyo amakukondani kwambiri nonsenu akakumbukira kumvera kwanu,+ komanso mmene munamulandirira ndi mantha ndiponso kunjenjemera.