2 Akorinto 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti ndikulemba zimenezi pofuna kudziwa ngati mulidi omvera m’zinthu zonse.+ 2 Akorinto 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiponso iyeyo amakukondani kwambiri nonsenu akakumbukira kumvera kwanu,+ komanso mmene munamulandirira ndi mantha ndiponso kunjenjemera.
15 Ndiponso iyeyo amakukondani kwambiri nonsenu akakumbukira kumvera kwanu,+ komanso mmene munamulandirira ndi mantha ndiponso kunjenjemera.