2 Atesalonika 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tiyeneradi kumayamika Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu+ abale. N’koyenera kutero chifukwa chikhulupiriro chanu chikukula+ kwambiri, ndipo chikondi cha aliyense wa inu kwa mnzake chikuwirikiza.+
3 Tiyeneradi kumayamika Mulungu nthawi zonse chifukwa cha inu+ abale. N’koyenera kutero chifukwa chikhulupiriro chanu chikukula+ kwambiri, ndipo chikondi cha aliyense wa inu kwa mnzake chikuwirikiza.+