Levitiko 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “‘Mkulu wa ansembe akafuna kukwatira, azikwatira namwali.+ Aefeso 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 chifukwa mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake+ monganso mmene Khristu alili mutu wa mpingo,+ pokhala mpulumutsi wa thupilo.
23 chifukwa mwamuna ndiye mutu wa mkazi wake+ monganso mmene Khristu alili mutu wa mpingo,+ pokhala mpulumutsi wa thupilo.