Aheberi 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yesu Khristu ali chimodzimodzi dzulo ndi lero, ndiponso mpaka muyaya.+