2 Akorinto 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pakuti ngakhale nditati ndidzitamandire+ mopitirirako muyezo za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa kuti tikulimbikitseni, osati kukupasulani,+ sindingachite manyazi.
8 Pakuti ngakhale nditati ndidzitamandire+ mopitirirako muyezo za ulamuliro umene Ambuye anatipatsa kuti tikulimbikitseni, osati kukupasulani,+ sindingachite manyazi.